Ezekiel 30:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, ulose ndipo ulengeze kuti zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: “ ‘Pepani, tsiku latsoka lafika!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, nenera, uziti, Atero Ambuye Yehova, Liritsani, Ha, tsikulo!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, nenera ndipo ulengeze zimene Ine Ambuye Yehova ndikunena. “ ‘Ufuwule mawu awa akuti, ‘Kalanga, tsiku lafika!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobadwa ndi munthu iwe, nenera, uziti, Atero Ambuye Yehova, Liritsani, Ha, tsikulo