Ezekiel 30:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe mwana wa munthu, ndathyola dzanja la Farao, mfumu ya ku Ejipito. Ona, sadalimange kuti lichire, ndipo sadalilimbitse ndi nsalu kuti lithe kugwiranso lupanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobadwa ndi munthu iwe, ndathyola dzanja la Farao mfumu ya Aejipito, ndipo taona, silinamangidwa kuti lipole, kulikulunga ndi nsalu, kulilimbitsa ligwire lupanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, ndathyola dzanja la Farao mfumu ya Igupto. Taona, silinamangidwe kuti lipole, ngakhale kulilimbitsa ndi nsalu kuti lithe kugwiranso lupanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wabadwa ndi munthu iwe, ndatyola dzanja la Parao mfumu ya Aigupto, ndipo taona, silinamangidwa kuti lipole, kulikulunga ndi nsaru, kulilimbitsa ligwire lupanga.