Ezekiel 30:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵamwaza Aejipito pakati pa mitundu ya anthu ndi kuŵabalalitsira ku maiko ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzamwaza Aejipito mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa m'maiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamwaza Aigupto pakati pa mitundu ya anthu ndikuwabalalitsira ku mayiko ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzamwaza Aaigupto mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa m'maiko.