Ezekiel 30:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzamwaza Aejipito pakati pa mitundu ya anthu, ndi kuŵabalalitsira ku maiko ambiri. Motero adzadziŵa kuti Ine ndine Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzamwaza Aejipito mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa mwa amitundu; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamwaza Aigupto pakati pa mitundu ya anthu, ndikuwabalalitsira ku mayiko ambiri. Motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzamwaza Aaigupto mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa mwa amitundu; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.