Ezekiel 30:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko la Ejipito lidzasanduka bwinja kupambana mabwinja onse opasuka. Mizinda yake idzakhala yopasuka kupambana mizinda ina yoonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzakhala opasuka pakati pa maiko opasuka, ndi midzi yake idzakhala pakati pa midzi yopasuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Dziko la Igupto lidzasanduka bwinja kupambana mabwinja ena onse opasuka, ndipo mizinda yake idzakhala yopasuka kupambana mizinda ina yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzakhala opasuka pakati pa maiko opasuka, ndi midzi yace idzakhala pakati pa midzi yopasuka.