Ezekiel 32:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku loyamba la mwezi wa khumi ndi chiŵiri, chaka cha khumi ndi chiŵiri cha ukapolo, Chauta adandipatsira uthenga uwu wakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali chaka chakhumi ndi chiwiri, mwezi wakhumi ndi chiwiri, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku loyamba la mwezi wa khumi ndi chiwiri, chaka chakhumi ndi chiwiri, Yehova anandiyankhula kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali caka cakhumi ndi ciwiri, mwezi wakhumi ndi ciwiri, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,