Ezekiel 32:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: Nkhondo ya mfumu ya ku Babiloni idzakufika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Ambuye Yehova, Lupanga la mfumu ya ku Babiloni lidzakudzera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Pakuti ndikunena Ine Ambuye Yehova kuti, “ ‘Lupanga la mfumu ya ku Babuloni lidzabwera kudzalimbana nawe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Ambuye Yehova, Lupanga la mfumu ya ku Babulo lidzakudzera.