Ezekiel 32:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uŵafunse kuti, ‘Kani ndinu okongola kupambana ena? Tsikirani ku manda pamodzi ndi ena onse osaumbalidwa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uposa yani m'kukoma kwako? Tsika, nuikidwe ndi osadulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ufunse kuti, ‘Ndani amene akukuposa kukongola? Tsikirani ku manda ndi kukhala pamodzi ndi anthu osachita mdulidwe.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uposa yani m'kukoma kwako? tsika, nuikidwe ndi osadulidwa.