Ezekiel 32:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwenso Farao, udzatswanyika ndipo udzagona pamodzi ndi anthu akufa osaumbalidwa, pamodzi ndi amene adaphedwa pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo udzathyoledwa pakati pa osadulidwa, nudzagona pamodzi ndi iwo ophedwa ndi lupanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwenso Farao, udzaphwanyidwa ndi kuyikidwa pakati pa anthu osachita mdulidwe, amene anaphedwa ndi lupanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo udzatyoledwa pakati pa osadulidwa, nudzagona pamodzi ndi iwo ophedwa ndi lupanga.