Ezekiel 32:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine Ambuye Chauta ndikuti, Ndikadzasonkhanitsa pamodzi anthu a mitundu yambiri, ndidzakuponyera khoka ndipo iwowo adzakugwira m'kombe mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Ndidzakuponyera khoka langa mwa msonkhano wa mitundu yambiri ya anthu, nadzakuvuulira m'khoka mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono Ine Ambuye Yehova ndikuti, “ ‘Pogwiritsa ntchito gulu la anthu a mitundu yambiri, ndidzakuponyera khoka langa ndi kukugwira mu ukonde wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Ndidzakuponyera khoka langa mwa msonkhano wa mitundu yambiri ya anthu, nadzakubvuulira m'khoka mwanga.