Ezekiel 32:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadzakuwononga, ndidzaphimba thambo, ndipo ndidzadetsa nyenyezi. Ndidzaphimba dzuŵa ndi mtambo, ndipo mwezi sudzaŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakukuzima iwe ndidzaphimba thambo, ndi kudetsa nyenyezi zake; ndidzaphimba dzuwa ndi mtambo, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikadzakuwononga, ndidzaphimba miyamba ndikudetsa nyenyezi zake. Ndidzaphimba dzuwa ndi mtambo, ndipo mwezi sudzawala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakukuzima iwe ndidzaphimba thambo, ndi kudetsa nye nyezi zace; ndidzaphimba dzuwa ndi mtambo, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwace.