Ezekiel 32:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndidzavutitsa mitima ya anthu a mitundu yambiri, pamene ndidzakupititsa ku ukapolo pakati pa mitundu ina, ku maiko amene sudaŵadziŵe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzavutanso mitima ya mitundu yambiri ya anthu, pakufikitsa Ine chionongeko chako mwa amitundu, m'maiko amene sunawadziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzasautsa mitima ya anthu a mitundu yambiri pamene ndidzakupititsa ku ukapolo pakati pa mitundu ya anthu, ku mayiko amene iwe sunawadziwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzabvutanso mitima ya mitundu yambiri ya anthu, pakufikitsa Ine cionongeko cako mwa amitundu, m'maiko amene sunawadziwa.