Ezekiel 33:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimodzimodzi ndikamchenjeza munthu wochimwa kuti adzafa, tsono iye nkuleka kuchimwako, namachita zolungama ndi zabwino,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndikanena kwa woipa, Udzafa ndithu: koma akabwerera iye kuleka tchimo lake, nakachita choyenera ndi cholungama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati ndiwuza munthu woyipa kuti, ‘Udzafa ndithu,’ tsono iye nʼkutembenuka kuleka machimo ake ndi kuyamba kuchita zimene Yehova afuna,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndikanena kwa woipa, Udzafa ndithu: koma akabwerera iye kuleka cimo lace, nakacita coyenera ndi colungama;