Ezekiel 33:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino akaleka kuchita zabwino, nayamba kumachita zoipa, adzafa nazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akabwerera wolungama kuleka chilungamo chake, nakachita chosalungama, adzafa m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu wolungama atembenuka ndi kuleka ntchito zake zolungama ndi kuyamba kuchita zoyipa, adzafa nazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akabwerera wolungama kuleka cilungamo cace, nakacita cosalungama, adzafa m'mwemo.