Ezekiel 33:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono inu am'banja la Israele, mumanena kuti, ‘Zimene Chauta amachitazi nzopanda chilungamo.’ Iyai, aliyense mwa inu Ine ndidzamuweruza potsata zochita zake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munati, Njira ya Ambuye siiyenera. Nyumba ya Israele inu, ndidzakuweruzani, yense monga mwa njira zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Aisraeli, mukunena kuti, ‘Zimene Ambuye amachita ndi zopanda chilungamo.’ Ayi, inu Aisraeli, Ine ndidzaweruza aliyense wa inu potsata ntchito zake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munati, Njira ya Ambuye siiyenera. Nyumba ya Israyeli inu, ndidzakuweruzani, yense monga mwa njira zace.