Ezekiel 33:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumadalira malupanga anu. Mumachita zonyansa, ndipo aliyense amachita chigololo ndi mkazi wa mnzake. Kodi dzikolo nkudzakhaladi lanu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mumatama lupanga lanu, mumachita chonyansa, mumaipsa yense mkazi wa mnansi wake; ndipo kodi mudzakhala nalo dziko cholowa chanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumadalira lupanga lanu, mumachita zinthu zonyansa, ndipo aliyense wa inu amachita chigololo ndi mkazi wa mnzake. Kodi inu nʼkulandira dzikoli?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mumatama lupanga lanu, mumacita conyansa, mumaipsa yense mkazi wa mnansi wace; ndipo kodi mudzakhala nalo dziko colowa canu?