Ezekiel 33:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye akaona mdani akubwera, amaliza lipenga kuti achenjeze aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakaona iye lupanga lilikudzera dziko, nakaomba lipenga ndi kuchenjeza anthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iyeyo amati akaona nkhondo ikubwera amaliza lipenga kuti achenjeze anthuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakaona iye lupanga lirikudzera dziko, nakaomba lipenga ndi kucenjeza anthu;