Ezekiel 33:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wina akalimva lipengalo, koma osasamala, ndipo mdani akabwera nkumupha, wadziphetsa ndi mtima wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wina, kumva adamva mau a lipenga, koma osalabadira, likadza lupanga, nilimchotsa, wadziphetsa ndi mtima wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wina aliyense akamva lipenga koma osasamala, mdani uja akabwera nʼkumupha, ndiye kuti wadziphetsa yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wina, kumva adamva mau a lipenga, koma osalabadira, likadza lupanga, nilimcotsa, wadziphetsa ndi mtima wace.