Ezekiel 33:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wadziphetsa yekha chifukwa choti sadasamale chenjezo. Akadasamala, akadapulumuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamva mau a lipenga, osawalabadira, wadziphetsa ndi mtima wake; akadalabadira, akadalanditsa moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamva kulira kwa lipenga koma sanalabadire. Ndiye kuti wadziphetsa yekha. Akanasamala kuchenjeza kwa mlonda akanapulumuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamva mau a lipenga, osawalabadira, wadziphetsa ndi mtima wace; akadalabadira, akadalanditsa moyo wace.