Ezekiel 34:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono Ine Ambuye Chauta ndikukuuzani kuti, Ineyo mwiniwake ndidzaweruza ndekha pakati pa inu nkhosa zonenepanu ndi zinzanu zoondazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake atero nao Ambuye Yehova, Taonani, Ine, Inedi ndidzaweruza pakati pa zoweta zonenepa, ndi zoweta zoonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Nʼchifukwa chake Ine Ambuye Yehova ndikuti: Taonani, Ine mwini wake ndidzaweruza pakati pa nkhosa zonenepa ndi nkhosa zowonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace atero nao Ambuye Yehova, Taonani, Ine, Inedi ndidzaweruza pakati pa zoweta zonenepa, ndi zoweta zoonda.