Ezekiel 34:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzachulukitsa zolima zao, mwakuti sadzafanso ndi njala m'dzikomo, ndipo choncho anthu a mitundu ina sadzaŵanyozanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzawautsira mbeu yomveka, ndipo sadzachotsedwanso ndi njala m'dzikomo, kapena kusenzanso manyazi a amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawapatsa zokolola zochuluka motero kuti sadzavutikanso ndi njala. Anthu a mitundu ina sadzawanyozanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzawautsira mbeu yomveka, ndipo sadzacotsedwanso ndi njala m'dzikomo, kapena kusenzanso manyazi a amitundu.