Ezekiel 34:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chambiko mumadya, zaubweya mumavala, ndipo nyama zonenepa mumapha, koma nkhosa osasamala konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukudya mafuta, muvala ubweya, mukupha zonenepa; koma simudyetsa nkhosa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumadya chambiko, mumadziveka zovala zaubweya, ndi kupha nyama zonenepa, koma simusamalira nkhosazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukudya mafuta, mubvala ubweya, mukupha zonenepa; koma simudyetsa nkhosa.