Ezekiel 34:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake abusa inu, imvani mau a Ine Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake, abusa inu, imvani mau a Yehova:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chake, inu abusa, tamvani zimene Ine Yehova ndikukuwuzani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace, abusa inu, imvani mau a Yehova: