Ezekiel 35:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu mudanena kuti, ‘Mitundu iŵiri ya anthu, Yuda ndi Israele, idzakhala yathu pamodzi ndi maiko ao omwe.’ Mudatero ngakhale kuti Ine Chauta ndinali nao m'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza wanena, Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi maiko awiri awa adzakhala anga, tidzakhala nao ngati cholowa chathu, angakhale Yehova anali komweko;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu munanena kuti, ‘Mitundu iwiri iyi ya anthu, Yuda ndi Israeli, pamodzi ndi mayiko awo omwe idzakhala yathu.’ Munanena chomwechi ngakhale kuti Ine Yehova ndinali momwemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza wanena, Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi maiko awiri awa adzakhala anga, tidzakhala nao ngati colowa cathu, angakhale Yehova anali komweko;