Ezekiel 35:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidamva zondinyoza zimene mudanena monyada. Ndidadzimvera ndekha zonse!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakamwa panu mwadzikuza pa Ine, ndi kundichulukitsira mau anu ndawamva Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu anu amene munayankhula monyada kundinyoza Ine ndinawamva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakamwa panu mwadzikuza pa Ine, ndi kundicurukitsira mau anu ndawamva Ine.