Ezekiel 35:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: Ndidzakusandutsani bwinja kotheratu, kotero kuti dziko lonse lapansi lidzakondwa nako kugwa kwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Pokondwerera dziko lonse ndidzakusanduliza lachipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine Ambuye Yehova ndikuti: Dziko lonse lapansi lidzasangalala pamene ndidzakusandutsani bwinja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Pokondwerera dziko lonse ndidzakusanduliza lacipululu.