Ezekiel 35:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munali adani a Israele nthaŵi zonse, ndipo munkalola kuti anthu ake aziphedwa pa nthaŵi ya mavuto ao, pa nthaŵi imene chilango chao chidafika pa chimake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza uli nao udani wosatha, waperekanso ana a Israele kumphamvu ya lupanga m'nthawi ya tsoka lao, mu nthawi ya mphulupulu yotsiriza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munali adani a Israeli nthawi zonse, ndipo munkalola kuti Aisraeli aphedwe pa nkhondo pa nthawi ya mavuto awo, pa nthawi imene chilango chawo chinafika pachimake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza uli nao udani wosatha, waperekanso ana a Israyeli ku mphamvu ya lupanga m'nthawi ya tsoka lao, mu nthawi ya mphulupulu yotsiriza;