Ezekiel 36:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwuza kuti, “Tsono iwe mwana wa munthu, ulalikire mapiri a ku Israele, unene kuti, Inu mapiri a ku Israele, imvani uthenga uwu wochokera kwa Ambuye Chauta:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, unenere kwa mapiri a Israele, uziti, Mapiri a Israele inu, imvani mau a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mwana wa munthu, yankhula kwa mapiri a Israeli ndipo unene kuti, ‘Inu mapiri a Israeli, imvani mawu a Yehova.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwe, wobadwa ndi munthu, unenere kwa mapiri a Israyeli, uziti, Mapiri a Israyeli inu, imvani mau a Yehova.