Ezekiel 36:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaŵalanga mokalipa chifukwa cha magazi a anthu amene iwo adakhetsa m'dzikomo, ndiponso chifukwa cha mafano amene iwo adaipitsa nawo dzikolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo ndinawatsanulira ukali wanga, chifukwa cha mwazi anautsanulira padziko, ndi chifukwa cha mafano analidetsa dziko nao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ndinawalanga chifukwa cha magazi amene anakhetsa mʼdzikomo, ndiponso chifukwa anayipitsa dziko ndi mafano awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo ndinawatsanulira ukali wanga, cifukwa ca mwazi anautsanulira padziko, ndi cifukwa ca mafano analidetsa dziko nao;