Ezekiel 36:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: Pamene ndidzachotsa machimo anu, ndidzaikamonso anthu m'mizindamo, ndipo ndidzamanganso nyumba pa mabwinja aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Tsiku loti ndikuyeretsani kukuchotserani mphulupulu zanu zonse, ndidzakhalitsa anthu m'midzimo; ndi pamabwinja padzamangidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine Ambuye Yehova ndikuti: Pa tsiku limene ndidzayeretse machimo anu onse, ndidzayikamonso anthu mʼmizinda yanu, ndipo ndidzamanganso nyumba pa mabwinja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Tsiku loti ndikuyeretsani kukucotserani mphulupulu zanu zonse, ndidzakhalitsa anthu m'midzimo; ndi pamabwinja padzamangidwa.