Ezekiel 36:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko limene lidaasanduka tsala, anthu azidzalimamonso. Kale aliyense wopita m'njira ankaliwona ngati chipululu, tsopano adzaona kuti nlolimidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi dziko lachipululu lidzalimidwa, chinkana linali lachipululu pamaso pa onse opitako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko limene linasanduka chipululu lizidzalimidwanso. Mʼmalo moti aliyense wopitamo alione dzikolo ngati chipululu tsopano adzaliona lolimidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi dziko lacipululu lidzalimidwa, cinkana linali lacipululu pamaso pa onse opitako.