Ezekiel 36:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ine Ambuye Chauta mau anga ndi aŵa: Ndidzaŵalolanso Aisraele kuti andipemphe zimene afuna kuti ndiŵachitire. Ndidzachulukitsa anthu ao ngati nkhosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Ichi chomwe adzandipempha a nyumba ya Israele ndiwachitire ichi, ndidzawachulukitsira anthu ngati nkhosa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine Ambuye Yehova ndikuti: Ndidzalolanso Aisraeli kuti andipemphe zoti ndiwachitire: Ndidzachulukitsa anthu awo ngati nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Ici comwe adzandipempha a nyumba ya Israyeli ndiwacitire ici, ndidzawacurukitsira anthu ngati nkhosa.