Ezekiel 36:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu, mapiri a ku Israele, mudzaphukanso nthambi, ndipo anthu anga Aisraele mudzaŵabalira zipatso, poti ali pafupi kubwerera kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu, mapiri a Israele, mudzaphukitsa nthambi zanu, ndi kubalira anthu anga Israele zipatso zanu, pakuti ayandikira kufika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma Inu mapiri a Israeli mudzaphukanso nthambi ndipo mudzawabalira zipatso anthu anga a Israeli, pakuti ali pafupi kubwerera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu, mapiri a Israyeli, mudzaphukitsa nthambi zanu, ndi kubalira anthu anga Israyeli zipatso zanu, pakuti ayandikira kufika.