Ezekiel 36:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndikusamala za inu, ndipo ndidzakukomerani mtima. Mudzalimidwanso ndi kubzalidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti taonani, Ine ndikhalira nanu kumodzi, ndipo ndidzakutembenukirani; ndipo mudzabzalidwa ndi kupaliridwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taonani, Ine ndili mbali yanu ndipo ndidzakukomerani mtima. Mudzalimidwa ndi kudzalidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti taonani, Ine ndikhalira nanu kumodzi, ndipo ndidzakutembenukirani; ndipo mudzabzalidwa ndi kupaliridwa,