Ezekiel 37:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mudzadziŵa kuti Ine ndine Chauta, ndikadzafukula manda anu ndi kukutulutsanimo, inu anthu anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova potsegula Ine kumanda kwanu, ndi kukweza inu kukutulutsani m'manda mwanu, anthu anga inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo inu, anthu anga, mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pamene ndidzafukula manda anu ndikukutulutsanimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine. Yehova potsegula Ine kumanda kwanu, ndi kukweza inu kukuturutsani m'manda mwanu, anthu anga inu.