Ezekiel 37:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono utenge ndodo ziŵirizo ndi kuzilumikiza kuti zikhale ngati ndodo imodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nuiphatikize wina ndi unzake ikhale mtengo umodzi m'dzanja lako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ulumikize ndodo ziwirizi kuti zikhale ndodo imodzi mʼdzanja lako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nuiphatikize wina ndi unzace ikhale mtengo umodzi m'dzanja lako.