Ezekiel 37:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu akwanu akakufunsa tanthauzo lake la zimenezi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a anthu a mtundu wako akanena ndi iwe, ndi kuti, Sutifotokozera nanga zitani izi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu a mtundu wako akadzakufunsa tanthauzo la zimenezi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a anthu amtundu wako akanena ndi iwe, ndi kuti, Sutifotokozera nanga zitani izi?