Ezekiel 37:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiyendetsa uku ndi uku pakati pa mafupawo. Mafupawo analitu ochuluka kwambiri m'chigwa chonsecho, ndipo anali ochita kuti gwaa kuuma kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anandipititsa pamenepo pozungulira ponse, ndipo taonani, anali aunyinji pachigwa pansi, ndipo anaumitsitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anandiyendetsa uku ndi uku pakati pa mafupawo. Mafupawo anali ochuluka kwambiri mʼchigwa monsemo ndipo anali owuma kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anandipititsa pamenepo pozungulira ponse, ndipo taonani, anali aunyinji pacigwa pansi, ndipo anaumitsitsa.