Ezekiel 37:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yao, motero onsewo adzakhala ndi mbusa mmodzi. Adzatsata malamulo anga, adzamvera mosamala malangizo anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yao, ndipo iwo onse adzakhala ndi mbusa mmodzi, adzayendanso m'maweruzo anga, nadzasunga malemba anga ndi kuwachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo, motero onsewa adzakhala ndi mʼbusa mmodzi. Iwo adzatsatira malamulo anga ndipo adzasamalira kusunga malangizo anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yao, ndipo iwo onse adzakhala ndi mbusa mmodzi, adzayendanso m'maweruzo anga, nadzasunga malemba anga ndi kuwacita.