Ezekiel 37:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo anthu a mitundu ina adzadziŵa kuti Ine Chauta Aisraele ndimaŵasandutsa oyera, chifukwa chakuti Nyumba yanga ili pakati pao mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amitundu adzadziwa kuti Ine ndine Yehova wakupatula Israele, pokhala pakati pao malo anga opatulika kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anthu a mitundu ina adzadziwa kuti Ine Yehova ndiye amene ndimasandutsa Israeli kukhala woyera, pamene malo anga opatulika adzakhala pakati pawo kwamuyaya!’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amitundu adzadziwa kuti Ine ndine Yehova wakupatula Israyeli, pokhala pakati pao malo anga opatulika kosatha.