Ezekiel 38:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zimene ndikunena Ine Ambuye Chauta ndi izi: Pa tsiku limenelo mumtima mwako mudzaloŵa maganizo ofuna kukonzekera kuchita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Ambuye Yehova, Kudzachitika tsiku ilo kuti m'mtima mwako mudzalowa zinthu, nudzalingirira chiwembu choipa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine Ambuye Yehova ndikuti: Pa tsiku limenelo mu mtima mwako mudzabwera maganizo ofuna kukonzekera kuchita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Ambuye Yehova, Kudzacitika tsiku ilo kuti m'mtima mwako mudzalowa zinthu, nudzalingirira ciwembu coipa,