Ezekiel 38:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umuuze kuti Ine Ambuye Chauta, ndikuti, Ndikudana nawe, iwe Gogi, kalonga wamkulu wa ku Meseki ndi ku Tubala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe, Gogi iwe, mfumu yaikulu ya Meseki ndi Tubala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umuwuze mawu a Ine Ambuye Yehova akuti, ‘Ine ndikudana nawe, iwe Gogi, kalonga wamkulu wa ku Mesaki ndi Tubala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nunenere motsutsana naye, uziti, Atero Ambuye Yehova, Taona, nditsutsana nawe, Gogi iwe, mfumu yaikuru ya Meseki ndi Tubala;