Ezekiel 39:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adzakhala akukwirira mitembo pa miyezi isanu ndi iŵiri, kuti ayeretse dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a nyumba ya Israele adzapititsa miyezi isanu ndi iwiri alikuwaika, kuti ayeretse dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nyumba ya Israeli idzakhala ikukwirira mitembo kwa miyezi isanu ndi iwiri ndi cholinga choyeretsa dziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a nyumba ya Israyeli adzapititsa miyezi isanu ndi iwiri alikuwaika, kuti ayeretse dziko.