Ezekiel 39:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popita m'dzikomo, azidzati wina akaona fupa la munthu, azidzaika chizindikiro pambali pake, mpaka fupalo litakwiriridwa m'chigwa cha gulu lankhondo la Gogi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo opitapitawo adzapitapita m'dziko, ndipo wina akaona fupa la munthu aikepo chizindikiro, mpaka oikawo aliika m'chigwa cha unyinji wa Gogi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Poyenda mʼdzikomo azidzati akaona fupa la munthu azidzayikapo chizindikiro pambali pake mpaka okumba manda atakalikwirira fupalo ku chigwa cha gulu lankhondo la Gogi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo opitapitawo adzapitapita m'dziko, ndipo winaakaona pfupa la munthu aikepo cizindikilo, mpaka oikawo aliika m'cigwa ca unyinji wa Gogi.