Ezekiel 39:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzadya nyama ya ankhondo amphamvu, ndipo mudzamwa magazi a akalonga a dziko lapansi. Onsewo adaphedwa ngati nkhosa zamphongo, anaankhosa, mbuzi ndiponso ngati ng'ombe zamphongo zonenepa za ku Basani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzadya nyama ya amphamvu, ndi kumwa mwazi wa akalonga a padziko, wa nkhosa zamphongo, wa anaankhosa, ndi wa mbuzi, ndi wa ng'ombe, zonsezi zonenepa za ku Basani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzadya mnofu wa anthu ankhondo amphamvu ndi kumwa magazi a akalonga a dziko lapansi. Onsewo anaphedwa ngati nkhosa zazimuna, ana ankhosa onenepa, mbuzi ndiponso ngati ngʼombe zazimuna zonenepa za ku Basani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzadya nyama ya amphamvu, ndi kumwa mwazi wa akalonga a padziko, wa nkhosa zamphongo, wa ana a nkhosa, ndi wa mbuzi, ndi wa ng'ombe, zonsezi zonenepa za ku Basana.