Ezekiel 39:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuzunguza ndi kukupirikitsira m'tsogolo. Ndidzakutenga kuchokera ku maiko akutali kumpoto, ndipo ndidzakutuma kuti ukalimbane ndi anthu okhala m'mapiri a ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzakutembenuza, ndi kukutsogolera, ndi kukweza iwe uchoke ku malekezero a kumpoto; ndipo ndidzadza nawe kumapiri a Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzakuzunguza ndi kukupirikitsira kutsogolo. Ndidzakutenga kuchokera kutali kumpoto ndi kukutumiza kuti ukalimbane ndi anthu a ku mapiri a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzakutembenuza, ndi kukutsogolera, ndi kukweza iwe ucoke ku malekezero a kumpoto; ndipo ndidzadza nawe ku mapiri a Israyeli;