Ezekiel 39:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaŵachita zimenezi chifukwa cha kunyansa kwao ndi machimo ao, ndipo ndidaŵafulatiradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinachita nao monga mwa kudetsedwa kwao, ndi monga mwa kulakwa kwao, ndipo ndinawabisira nkhope yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinawachita zimenezi chifukwa cha kunyansa kwawo ndi zolakwa zawo, ndipo ndinawabisira nkhope yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinacita nao monga mwa kudetsedwa kwao, ndi monga mwa kulakwa kwao, ndipo ndinawabisira nkhope yanga.