Ezekiel 39:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake ndidzathyola uta wa ku dzanja lako lamanzere, ndipo ndidzagwetsa mivi ya ku dzanja lako lamanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzakantha uta wako kuuchotsa m'dzanja lako lamanzere, ndi kutayitsa mivi yako kudzanja lako lamanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Ine ndidzathyola uta wa mʼdzanja lako lamanzere ndipo ndidzagwetsa mivi ya mʼdzanja lako lamanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzakantha uta wako kuucotsa m'dzanja lako lamanzere, ndi kutayitsa mibvi yako ku dzanja lako lamanja.