Ezekiel 4:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uyesekonso makapu aŵiri a madzi, kuti akhale chakumwa chako cha tsiku ndi tsiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uzimwanso madzi monga mwa muyeso, limodzi la magawo asanu ndi limodzi la hini; uzimwako tsiku ndi tsiku pa nthawi yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uyezenso zikho ziwiri zamadzi ndipo uzimwa tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uzimwanso madzi monga mwa muyeso, limodzi la magawo asanu ndi limodzi la hini; uzimwako tsiku ndi tsiku pa nthawi yace.