Ezekiel 4:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adati, “Buledi ameneyu ndiye chifaniziro cha chakudya chodetsedwa chimene Aisraele azidzadya ku maiko achilendo kumene ndidzaŵapirikitsire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati, Motero ana a Israele adzadya chakudya chao chodetsedwa, mwa amitundu kumene ndidzawaingitsirako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anati, “Chimodzimodzi anthu a Israeli adzadya chakudya chodetsedwa ku mayiko achilendo kumene Ine ndidzawapirikitsira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati, Motero ana a Israyeli adz adya ca kudya cao codetsedwa, mwa amitundu kumene ndidzawaingitsirako.